Jungle - Julia скачать mp3

03:15
7.53 Мб
320 Кб/с
889
Скачать MP3

Смотреть клип Julia

Текст песни Julia

anandipatsa chikondi chosowa mwana mkazi ine chim'tima kuda bii monga wakhungu kulephera kupenya ine uchitsilu chim'chenga m'maso waa ndinapusa ndi mtima wanga ouma monga mwala ine kupwalala pozindikira linali tsiku ankanka kwao kumangoni ine nkhawa bii juila julia usatelo julia julia bwerera ndikagona ndimangolota kuti mwina iye adzabweranso nthawi zambiri ndikakhala ndimalira kunong'oneza bondo ndikanadziwa nkanamupatsa chikondi changa chonse ndi mtima wanga wonse nkanamupatsa moyo wanga bwezi ndithu mpaka lero tikadali limodzi juila julia juila julia usatelo juila julia julia julia bwerera ambirife tikapeza chikondi timatayilira timayiwalanso kuti n'cham'tengo wapatali ukapeza chikondi n'chofunika kuchisamalira poti monga dzira sichichedwa kusweka

Похожие треки

Треки альбома

--:--:-- / --:--:--